ECOGEN MALAWI’s Post

Ikakhala nkhani ya moto wophikira kapena feteleza kumunda, mtima wanu uzidekha. Kungokhala ndi biogas system, basi zonse zayera. Tiyimbireni kuti mumve zambiri. #Biogas #Biofertilizer

  • No alternative text description for this image

What's the associated cost to install this system?

Hazvinei Mang'anda

Programs Manager |SynbioAfrica Deputy Ambassador| Research Scholar|Wellness and Support Coordinator Women in Synthetic Biology Africa (WiSBA)

2mo

Mtima wanga dekha poti kuli biogas ..Great work ECOGEN MALAWI

Like
Reply
See more comments

To view or add a comment, sign in

Explore topics